Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi m’dziko muno Casper Chalera wamwalira. M’neneri wa nthambiyi m’dziko muno, a Peter Kalaya, atsimikizira YFM…
Anthu 7 amwalira pa ngozi ku Blantyre
Amayi asanu ndi awiri amwalira pa ngozi ya galimoto lolemba mu msewu wa Chileka m’boma la Blantyre. M’neneri wa polisi…
Dr Usi apita ku Morocco
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wanyamuka m’dziko muno lero ulendo wa ku Morocco komwe akakhale nawo…
MCP sibwera ku msonkhano waukulu, yatero UDF
Chipani cha United Democratic (UDF) chatsimikiza kuti chasintha ganizo lake loyitana chipani cholamula cha Malawi Congress (MCP) kuti chidzakhale nawo…
Survivors call for collaboration in tackling childhood cancer
Government and all the stakeholders in health sector, have been asked to collaborate in intensifying sensitization messages about childhood cancer.…
Apolisi anjata bambo pomuganizira mulandu wogwilira
Bambo wa zaka 25, Clever Makina, ali m’manja mwa apolisi ku Blantyre pomuganizira kuti anagonana ndi msungwana wa zaka 16…
Musalowetse ndale pa mapemphero, Arkiepiskopi Msusa achenjeza ansembe
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika mu Arkidayosizi ya Blantyre, Arkiepiskopi Thomas Msusa, achenjeza ansembe kuti asalore anthu a ndale kugwiritsa…
DoDMA yati zipangizo za kunja zikuchedwetsa ntchito yokonzanso zoonongwedwa ndi namondwe
Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yati ntchito zokonzanso zinthu zomwe zidawonongeka kaamba ka a namondwe, zikumachedwa kutha…
Journalists urged to champion environmental conservation
Malawi Environmental Protection Authority (MEPA) has urged science journalists to do more in championing environmental conservation initiatives. Tawonga Mbale, MEPA…
Alamulidwa zaka 18 kamba kogwililira mwana
Bambo wa zaka 25, Foster Mathewe Saidi, wayamba kugwira ukayidi wa zaka 18 ku ndende kaamba komugona msungwana wa zaka…
DPP’s Makwinja elected Blantyre City Mayor
Democratic Progressive Party (DPP) councilor, Joseph Makwinja has been elected as new mayor for Blantyre City. Makwinja won with 16…
Man jailed 40 years for defiling 8 year-old nice
The High Court sitting in Kasungu on Tuesday, convicted and sentenced Christopher Simoni, 28, to 40 years imprisonment with hard…