Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), lati lachinayi likudzali lichititsa ziwonetsero mu nzinda wa Lilongwe zosonyeza…
Nthambi ya ndende ilimbikitsa ntchito za manja
Nthambi ya ndende m’dziko muno yati kuphunzitsa anthu omwe akugwira ukaidi luso la ntchito za manja ndi njira imodzi yomwe…
Mkumano usonkhanitsa achinyamata 500 — NYCOM
Bungwe la National Youth Council of Malawi (NYCOM) lati zonse zokhudza mkumano wawukulu wa achinyamata mdziko muno omwe uyambe lolemba…
CDEDI yati kalembera wa chisankho aime kaye
Bungwe la Centre for Democracy and Economic Initiatives (CDEDI) lapempha bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) kuti lisayambe gawo lachiwiri…
Boma ladzipereka pofuna kuthetsa njala
Nduna yowona za malimidwe a Sam Kawale yati boma ladzipereka pofuna kuthetsa njala mdziko muno pogwiritsa ntchito ulimi wothilira. Iwo…
UDF sinalowe mu mgwirizano ndi chipani chilichonse
Mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF), Atupele Muluzi, watsimikizira akuluakulu a chipanichi kuti palibe chipani chilichonse chomwe akukambirana…
Chakwera wakhazikitsa komiti yapadera yoti ifufuze za ngozi ya ndege
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wakhazikitsa komiti yapadera yoti ifufuze zokhudza ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri kwa…
Bungwe la MEC lati zipani zisade nkhawa
Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) latsutsa nkhawa za zipani zotsutsa m’dziko muno kuti bungweri liribe kuthekera koyendetsa chisankho cha…
Boma ladandaula ndi kuchepa kwa chidwi cha olemba ntchito
Unduna wa za umoyo wadandawula kaamba kakuchepa kwa chidwi chomwe anthu olemba anzawo ntchito akumayika pofuna kuti anthu awo adzikhala…
Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi Casper Chalera wamwalira
Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi m’dziko muno Casper Chalera wamwalira. M’neneri wa nthambiyi m’dziko muno, a Peter Kalaya, atsimikizira YFM…
Anthu 7 amwalira pa ngozi ku Blantyre
Amayi asanu ndi awiri amwalira pa ngozi ya galimoto lolemba mu msewu wa Chileka m’boma la Blantyre. M’neneri wa polisi…
Dr Usi apita ku Morocco
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wanyamuka m’dziko muno lero ulendo wa ku Morocco komwe akakhale nawo…