Amayi asanu ndi awiri amwalira pa ngozi ya galimoto lolemba mu msewu wa Chileka m’boma la Blantyre. M’neneri wa polisi…
Dr Usi apita ku Morocco
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wanyamuka m’dziko muno lero ulendo wa ku Morocco komwe akakhale nawo…
MCP sibwera ku msonkhano waukulu, yatero UDF
Chipani cha United Democratic (UDF) chatsimikiza kuti chasintha ganizo lake loyitana chipani cholamula cha Malawi Congress (MCP) kuti chidzakhale nawo…
Wotayira mwana mchimbudzi agamulidwa miyezi 6
Wolemba Lauryn M’banga Bwalo la milandu m’boma la Chikwawa lagamula kuti Maria Akimu wa zaka 20 akakhale kundende kwa miyezi…
Abambo atatu awamanga kamba kokupha m’bale wawo
Abambo atatu awamanga m’boma la Dowa powaganizira kuti apha mchimwene wawo Howard Yolamu pomubaya ndinso kumukhapa potsatira mkangano wokhudza malo…
Apolisi anjata bambo pomuganizira mulandu wogwilira
Bambo wa zaka 25, Clever Makina, ali m’manja mwa apolisi ku Blantyre pomuganizira kuti anagonana ndi msungwana wa zaka 16…
Boma alipempha kuti lisinthe malamulo otetedza nyama
Wolemba Emmanuel Yokonia Bungwe la National Youth Network on Climate Change lapempha boma kuti lisinthe malamulo omwe anakhazikitsidwa mchaka cha…
Musalowetse ndale pa mapemphero, Arkiepiskopi Msusa achenjeza ansembe
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika mu Arkidayosizi ya Blantyre, Arkiepiskopi Thomas Msusa, achenjeza ansembe kuti asalore anthu a ndale kugwiritsa…
Boma la Tonse lalephera watero Mutharika
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP), Arthur Peter Mutharika wati boma la…
Mlandu wa a Bushiri wayima kaye
Oweruza milandu wa bwalo la Chief Resident Magistrate ku Lilongwe a Madalitso Chimwaza wati adzapereka chigamulo mtsogolomu pa mlandu omwe…
Alamulidwa zaka 18 kamba kogwililira mwana
Bambo wa zaka 25, Foster Mathewe Saidi, wayamba kugwira ukayidi wa zaka 18 ku ndende kaamba komugona msungwana wa zaka…
Mlandu wa a Bushiri upitirira Lachitatu
Wolemba Emmanuel Yokonia Woyimira anthu pa milandu, Wapona Kita, wati ndi wokhutira ndi m’mene ikuyendera ndondomeko yofunsa mafunso mboni ya…